similarity float32 1.04 1.25 ⌀ | French stringlengths 1 500 | Chichewa stringlengths 3 500 |
|---|---|---|
1.248794 | [Qu'ils sachent], cependant, qu'un seul jour, auprès de ton Seigneur, équivaut à mille ans de ce que vous comptez. | Ndipo ndithu tsiku limodzi kwa Mbuye wako lili ngati zaka chikwi chimodzi mukawerengedwe kanu. |
1.247015 | Ton Seigneur dit aux anges, " Je vais créer l'être humain à partir de l'argile. | " (Akumbutse) pamene Mbuye wako adanena kwa angelo: "Ine ndilenga munthu kuchokera ku dothi, (yemwe ndi Adam)." |
1.245635 | Les gens des cités sont-ils sûrs que Notre châtiment rigoureux ne les atteindra pas le jour, pendant qu'ils s'amusent? | "Kodi anthu a m'mizinda (iyo momwe muli anthu oipa) ali ndi chitetezo cholimba kuti chilango chathu sichingawadzere usiku iwo ali mtulo? |
1.243003 | Ne vous avons-nous pas créés d'un peu d'eau, | Kodi sitidakulengeni kuchokera ku madzi |
1.242356 | 9- Dis: "Renierez-vous [l'existence] de celui qui a créé la terre en deux jours | "Nena: "Kodi inu mukumkanira yemwe adalenga nthaka mmasiku awiri (okha)? |
1.241623 | " Et ils t'interrogent sur la menstruation des femmes. - Dis: "C'est une incommodité. | "Ndipo (iwo) akukufunsa za kukhala malo amodzi ndi azimayi panthawi imene akusamba, auze (kuti): "Zimenezo ndizovulaza (ndiponso ndiuve). |
1.241225 | [Mais] vous êtes très peu reconnaissants. | Koma kuyamika kwanu (kwa Yemwe adakupatsani zimenezi) nkochepa kwambiri. |
1.238777 | Ton Seigneur dit aux anges, " Je vais créer l'être humain à partir de l'argile." | " (Akumbutse) pamene Mbuye wako adanena kwa angelo: "Ine ndilenga munthu kuchokera ku dothi, (yemwe ndi Adam)." |
1.232482 | Si nous avions voulu, nous aurions pu envoyer à chaque communauté un avertisseur. | "Ndipo tikadafuna, tikadatuma mchenjezi wawowawo m'mudzi uliwonse, (koma tatuma Muhammad {s.a.w} kuti akhale mchenjezi wa onse). |
1.231088 | " Il n'est pas interrogé sur ce qu'Il fait, mais ce sont eux qui devront rendre compte (de leurs actes). " | "Safunsidwa pa zimene akuchita, koma iwo adzafunsidwa. |
1.230849 | Ainsi le matin, plus rien n'était visible en dehors de leurs demeures. | Kenako adali osaonedwanso, kupatula nyumba zawo (ndizimene zidatsalira). |
1.230272 | Revenez-y jusqu'à ce que vous en soyez satisfait (e). | Pali Bwezerani batani kwa inu ngati sindicho kuti adzathe kuchita izo mpaka inu wokhutira ndi chifukwa. |
1.229425 | Peut-être se rappellera-t-il ou (Me) craindra-t-il ? ils dirent: " Ô notre Seigneur, nous craignons qu'il ne nous maltraite indument ou qu'il dépasse les limites ." | " (Iwo) adati: "Mbuye wathu ndithu ife tikuopa kuti angatimbwandire kapena kutipyolera malire (tisananene kanthu)." |
1.228276 | Ce n'est que la pure vérité). | Ina ukweli, ila inauma! |
1.227006 | Et sur la terre il y a des Signes pour ceux qui ont la certitude de la foi, | M'nthaka muli zizindikiro kwa Otsimikiza, (Zosonyeza kuti Mulungu alipo). |
1.226868 | Ainsi en sera-t-il de tous ceux qui se font les serviteurs des sens. | Ndithu m'zimenezo muli malingaliro kwa kapolo aliyense wotembenukira (kwa Allah). |
1.226655 | "pour celui d'entre vous qui veut suivre le chemin droit. | "Kwa yemwe mwa inu akufuna kuyenda mu njira yoongoka. |
1.225514 | et leurs prières, s'associeront à sa peine. | Mapemphero awo amangokhala amwambo ndipo amasiya kucheza ndi olambira anzawo. |
1.22505 | Dans tout cela il y a des signes pour tout homme plein d'endurance et de reconnaissance." | Ndithu m'zimenezo muli zizindikiro kwa yense wopirira, wothokoza. |
1.2249 | afin que, si l'une oublie, l'autre puisse rappeler le fait.." | ..." kuti ngati mmodzi mwa iwo (akazi awiriwo) angaiwale mmodzi wawo akumbutse winayo...." |
1.224809 | "Avant, c'était lui (Kadhafi) et le peuple était faible. | Ndipo Firiaun ndi amene adalipo iye Asadabadwe, ndi khamu la anthu amidzi Yotembenuzidwa (anthu a Luti) adadza Ndi machimo (akulu). |
1.224648 | Et il y avait dans la ville un groupe de neuf personnes qui semaient le désordre sur la terre et ne se rétablissaient pas. | "Ndipo m'mudzimo adalipo anthu asanu ndi anayi omwe amaononga pa dziko, ndipo samakonza (chilichonse koma kuchiononga). |
1.224605 | Et Notre Seigneur le Tout Miséricordieux, c'est Lui dont le secours est imploré contre vos assertions" (18). | "Ndipo Mbuye wathu ndi (Allah) Wachifundo chambiri; Wopemphedwa chithandizo pa zimene mukusimbazo." |
1.224537 | [11:103] Ceci devrait être une leçon pour ceux qui craignent le châtiment de l'Au-delà. | "Ndithu m'zimenezi muli lingaliro kwa yemwe akuopa chilango cha tsiku lachimaliziro. |
1.224464 | Jeanne et d'autres croyantes ont fait pour leur Seigneur ce qu'elles ont pu. | Jowana ndi akazi ena okhulupirika ankachita zimene akanatha pothandiza Ambuye wawo |
1.224081 | Agrandissez-les au fur et à mesure. | Ndipo kotero muwaike iwo pansi - ndipo mochuluka kwambiri. |
1.223417 | Il est certes parmi les injustes. " | Ndithu iye ndi m'modzi wa ochita zoipa." |
1.222598 | Voilà ce que j'aime le président latino-américain. | Ndicho chimene ine ndimakonda za pulezidenti Latin American. |
1.222361 | Il n'est pas de mise que ce Qur'ān puisse être inventé de la part d'un autre qu'Allah. | "Ndipo sikotheka Qur'an iyi kukhala yopekedwa, yosachokera kwa Allah (monga momwe munenera). |
1.222306 | s [o] est satisfaite. | kotero kuti adzasangalala, |
1.22204 | C'est Toi notre protecteur, et non pas eux. | Inu ndinu Mtetezi wathu, osati iwo. |
1.222007 | Dis: " La vérité est arrivée, et le mensonge n'a pu commencer quoi que ce soit, ni le répéter. " | "Nena: "Choonadi chadza (chisilamu); ndipo chabodza (chipembedzo cha mafano) sichidzetsa zachilendo, ndiponso sichibwerera (kukhala ndi nyonga monga kale)." |
1.221177 | Et nous avons créé l'homme et savons ce qu'est l'esprit qui entre en lui, et nous sommes plus proches de lui que [his] tonus musculaire. | Ndithu tidamulenga munthu, ndipo Ife Tikudziwa zimene mtima wake Ukumunong'oneza; ndipo Ife tili pafupi Ndi iye kuposa mtsempha wam'khosi Mwake. |
1.22111 | [7] Mais aussi le peuple de Noé, son fils, Thamûd, Coré et d'autres. | ""Monga chikhalidwe cha anthu a Nuh, Âdi, Samudi ndi anthu omwe adadza pambuyo pawo. |
1.220963 | Eh bien ! non ! [l'Homme] n'a pas encore accompli ce que [le Seigneur] lui a ordonné. | Ayi ndithu (munthu) sanakwaniritsebe Zimene adamulamula Mbuye wake (Mulungu chingakhale Wakhala nthawi yaitali padziko Lapansi). |
1.220884 | Montrez-moi ce qu'ils ont créé de la Terre; ou bien ont-ils une part [de gestion*] dans les cieux ? | Tandionetsani, ndimbali iti ya nthaka adalenga; kapena iwo ali ndi gawo m'thambo; (gawo lakulenga thambo?) |
1.220141 | Le peuple des fils d'Israël est plus nombreux et plus fort que nous." | Ana a Isiraeli achuluka kwambiri ndipo ndi amphamvu kuposa ife.' |
1.219522 | Pour tout cela, sa colère ne s'est pas détournée, et sa main est encore étendue. | Chifukwa cha zonsezi, mkwiyo wake sunabwerere, ndipo dzanja lake lidakali lotambasula. |
1.219378 | Les yeux de tous s'attendent à toi, et tu leur donnes leur nourriture en son temps. | Maso a onse ayembekeza Inu; Ndipo muwapatsa cakudya cao m'nyengo zao. |
1.219268 | et leurs descendants se maintiendront devant toi. | zidzukulu zawo zidzakhazikika pamaso panu." |
1.218885 | Car Nous avons mis à l'épreuve ceux qui les ont précédés. | Ndipo ndithu, tidawayesa amene adalipo Patsogolo pawo. |
1.218432 | " La vie de ce monde est pour ceux qui ne croient pas et qui se moquent des croyants. | "Moyo wa pa dziko lapansi wakometsedwa kwa amene sadakhulupirire, ndipo amawachitira chipongwe amene akhulupirira. |
1.218276 | Président des États-Unis d'Amérique, qui est devenu 20. | Purezidenti wa United States of America, amene anakhala 20. |
1.217414 | Vois-tu celui qui traite de [......] la Rétribution? | "Kodi wamuona yemwe akutsutsa za mphoto (ndi chiwerengero cha tsiku lachimaliziro)? |
1.216272 | Ceux-ci, dans les Jardins, s'interrogent entre eux | " (Iwo) adzakhala m'minda (yosasimbika kukongola kwake) akufunsana wina ndi mnzake, |
1.215724 | Et lorsqu'ils retournaient dans leurs familles, ils faisaient des blagues sur les croyants. | "Ndipo akabwerera kwa anzawo amabwerera akusangalala (ndi kunyozedwa kwa okhulupirira); |
1.215463 | Pourtant, Steve B. n'est pas allé en prison ce jour-là. | Komabe Steve B. sanapite kundende tsiku limenelo. |
1.21526 | et quand tu m'as rappelé auprès de toi, c'est toi qui les observais, car tu es témoin de toute chose. | Koma pamene mudanditenga, Inu ndiye mudali Muyang'aniri pa iwo; ndipo Inu ndinu Mboni ya chilichonse." |
1.215183 | Et Allah est suffisant en tant que Défenseur. | Ndipo Allah akukwanira kukhala Mtetezi. |
1.214963 | Le Jour où Nous susciterons un témoin de chaque communauté, il n'y aura pas d'indulgence pour les mécréants, et ils n'auront pas d'excuses à faire valoir. | "Ndipo (akumbutse za) tsiku lomwe tidzautsa mboni mu mtundu uliwonse; kenako sikudzaloledwa, kwa amene sadakhulupirire, (kupereka madandaulo) ndipo iwo sadzauzidwa kuti afunefune chiyanjo cha Allah (koma chilango basi). |
1.214933 | Le meilleur d'entre nous, c'est celui qui craint le plus ALLAH. | Ndipo malekezero abwino adzakhala a wanthu owopa (Allah). |
1.214333 | (53) Ce ne sera qu'un seul Cri, et voilà qu'ils seront tous amenés devant Nous. | "Sipadzakhala (china) koma mkuwe umodzi basi; adzangozindikira iwo onse atabweretsedwa patsogolo Pathu. |
1.214204 | c'est là, en vérité, la parole d'un noble Envoyé, | "Ndithudi iyi (Qur'an) ndiliwu la mthenga wolemekezeka (Jibril). |
1.214063 | et par trois cours d'eau, | pamadzi anakhala mpheta zitatu. |
1.214058 | Ne vous avons-nous pas créés d'un peu d'eau, | Kodi sitidakulengeni kuchokera Kumadzi onyozeka, (madzi ambewu ya Munthu)? |
1.213725 | " Et lorsque ton Seigneur dit aux anges: " Je vais établir un vice-roi sur la terre " Et c'est ce qui s'est passé. | " (Akumbutse) pamene Mbuye wako adanena kwa angelo: "Ine ndilenga munthu kuchokera ku dothi, (yemwe ndi Adam)." |
1.213601 | Si tu es docile à la parole du Seigneur en toutes les choses que je te prescris aujourd'hui d'observer, | Koma kudzakhala, ngati simvera mau a AMBUYE Mulungu wako, kuti usamalire kucita malamulo ake onse ndi malamulo ake, amene ndikuuzani lero; kuti matemberero onsewa adzakugwerani, ndi kukupezani: |
1.213588 | Je pense que ça devrait être sur le site de tout le monde, Patric. | Ndikuganiza kuti ziyenera kukhala patsamba la aliyense, Patric. |
1.212878 | S'il s'en trouve mille, ils en vaincront deux mille, avec la permission d'Allah. | Ngati alipo mwa inu chikwi chimodzi, adzagonjetsa zikwi ziwiri, mwachilolezo cha Allah. |
1.212633 | " Nous sommes des compagnons de travail pour votre joie " (2 COR. | "Ndife antchito anzanu kuti mukhale ndi chimwemwe." - 2 AKOR. |
1.212508 | Elle a sept portes; à chacune se tiendra une troupe d'entre eux. | "Ili ndi makomo asanu ndi awiri; khomo lililonse lili ndi gawo logawidwa mwa iwo. |
1.212252 | Lorsqu'il eut atteint sa maturité et la force de l'âge, Nous lui avons donné sagesse et science. | "Ndipo (Mûsa) pamene adakula nsinkhu wake ndi kulingana bwino tidampatsa nzeru ndi maphunziro. |
1.212036 | Margarita, par exemple, devait à présent chercher du travail. | Mwachitsanzo, Margarita tsopano anafunika kupeza ntchito. |
1.211971 | Entrez par les portes de l'enfer afin d'y rester éternellement. | "Lowani m'makomo a Jahannam; mukhala mmenemo nthawi yaitali. |
1.211772 | Dis: " La connaissance n'est qu'auprès de Dieu, et moi je ne suis qu'un avertisseur explicite ." | Nena (iwe MtumikijSAW}): "Ndithu Kudziwa (kwa izi) nkwa Mulungu yekha: Ndipo ndithudi ine, ndine mchenjezi Wowonekera." |
1.211766 | Je veux juste d'autres familles africaines à apprendre de cela. | Ndikungofuna kuti mabanja ena a ku Africa adziwepo izi. |
1.211675 | Et lorsqu'un mal atteint l'homme, celui-ci implore son Seigneur et s'en remet à Lui. | "Ndipo masautso akampeza munthu, amapempha Mbuye wake ndi kutembenukira kwa Iye (pomwe chikhalirecho adali kumnyoza). |
1.211535 | As-tu vu ce que tu as (encore) fait ! | Kodi siukuwaona awo amene achita |
1.21128 | Je n'ai donc pas besoin d'inclure - ou. entre les chiffres? | Chifukwa chake sindikufunika kuphatikiza - kapena. pakati pa manambala? |
1.211155 | C'est cela le très grand succès. | "Ndithu izi (zimene Allah waika m'Munda wamtendere) ndiko kupambana kwakukulu. |
1.211131 | Rappel (le Coran), et craint le Tout Miséricordieux, malgré qu'il ne Le voit pas. | Ndithu, kuchenjeza kwako Kupindulira amene watsatira Qur'an ndi kumuopa (Mulungu) Wachifundo ngakhale sakumuona. |
1.211112 | des personnes qui n'affichent pas leur Seigneur, | [Ndipo ali nacho anthu okanira Mbuye wawo |
1.210785 | Ils (eux deux) se dirigent vers l'entrée des pistes. | Ndipo (maiko) awiriwa ali m'njira zoonekera, (momwe Aquraish amadutsa pa maulendo awo). |
1.210708 | Salomon lui demande alors la sagesse et l'intelligence. | Solomo anapempha nzeru, chonde mafumu pemphani nzeru. |
1.21065 | " Il en est ainsi parce qu'Allah est la Vérité, et que tout ce qu'ils invoquent en | "Izi nchifukwa chakuti Allah, Iye Ngoona; ndipo zomwe akuzipembedza kusiya Iye, nzachabe. |
1.210564 | Elle va vous tuer jusqu'à ce que vous soyez mort (de stupéfaction). | Kenako adzakupatsani imfa (ikakwana nthawi yanu yofera). |
1.210468 | Quelqu'un qui vient à son Seigneur coupable subira l'Enfer, dans lequel il ne meurt jamais, ni ne reste en vie. | "Ndithu amene adzadze kwa Mbuye wake uku ali wamachimo, adzapeza moto wa Jahannam; sadzafa m'menemo, ndipo sadzakhalanso ndi moyo wabwino. |
1.210297 | Je déteste jouer aux dieux de Google autant que n'importe qui d'autre. | Ndimadana kusewera ndi milungu ya Google monga wina aliyense. |
1.210034 | et nous mettent mal à l'aise, | Ndipo iwo akutikwiitsa; |
1.209878 | Par exemple, c'est vrai que vous vivez ici à Paris depuis de nombreuses années?" | Mwachitsanzo, ndizowona kuti mwakhala kuno ku Paris kwazaka zambiri?" |
1.209855 | Car le Fils de l'homme doit venir dans la gloire de son Père, avec ses anges; et alors il rendra à chacun selon ses œuvres. | Mwana wa Munthu adzabwera mu ulemerero wa Atate wake limodzi ndi angelo ake, ndipo pomwepo mphoto kwa munthu aliyense monga mwa ntchito zake. |
1.209815 | Il a porté l'éternité de leur châtiment. | Iye anawayika chitonzo chamuyaya. |
1.209556 | Ton Seigneur s'est adressé aux anges par voie d'inspiration, leur disant: "Je suis avec vous. | " (Kumbukira) pamene Mbuye wako anawauza angelo kuti: "Ine ndili pamodzi nanu (pokulimbikitsani ndi chithandizo Changa). |
1.208844 | Et s'il est du nombre des gens de la droite, il sera | "Ndipo ngati adali mmodzi wa anthu akudzanja lamanja, |
1.208699 | Faire partie de cette famille est tout ce que je pourrais demander. | Kukhala m'modzi wabanja lino ndi zonse zomwe nditha kupempha. |
1.208667 | Car Toi, Seigneur, tu es l'aide de ceux qui n'ont pas d'aide, | A Chakwera inu bwanji osanthandiza. |
1.208348 | Dis: " La connaissance n'est qu'auprès de Dieu, et moi je ne suis qu'un avertisseur explicite ." | "Nena (iwe Mtumiki{s.a.w}): "Ndithu kudziwa (kwa izi) nkwa Allah yekha, ndipo ndithudi ine, ndine mchenjezi wowonekera." |
1.208242 | Il a dit que c'était si bien le jour où ils ont été créés | Anakukonzera zimenezi pa tsiku limene unalengedwa. |
1.207787 | Nous étions là le matin de la résurrection. | Tinali kumeneko m'maŵa wa chiukiriro. |
1.207505 | Et gare à celles qui se trouvent sur son chemin, le châtiment sera sans pitié. | Khululukirani amene alapa ndi kutsatira njira Yanu; ndipo apewetseni ku chilango cha Jahena!" |
1.207352 | de jouissance ainsi que leurs ancêtres au point qu'ils en ont oublié le | Koma mudawasangalatsa iwo ndi makolo awo kufikira adaiwala malangizo (Anu). |
1.207187 | Il vaut la peine de vous presser, avant l'arrivée des mécréants." | Musati mudzimange goli nokha ndi osakhulupirira." |
1.207056 | D'entre eux, Nous avons fait surgir douze chefs." | "Ndipo tidawagawa iwo m'mafuko khumi ndi awiri (osiyanasiyana) monga mitundu ikuluikulu. |
1.207054 | Et la cinquième attestation, qu'il appelle la malédiction d'Allah sur lui s'il est du nombre des menteurs. | "Ndipo kachisanu (alumbire) kuti matembelero a Allah akhale pa iye ngati (iye) ali m'modzi mwa onama. |
1.207021 | Ensuite, Nous vous avons pardonné, dans l'espoir que vous soyez reconnaissants. | "Kenako tidakukhululukirani pambuyo pa zimenezo, kuti muthokoze (mtendere wa Allah). |
1.206602 | En vérité, ton Seigneur décidera entre eux par Son jugement, et Il est le Puissant, l'Omniscient. | "Ndithu Mbuye wako adzalamula pakati pawo ndi chiweruzo chake (choona); ndipo Iye Ngwamphamvu zoposa Ngodziwa chilichonse. |
1.206551 | Car celui d'entre vous tous qui est le plus petit, c'est celui-là qui est grand." | Nakuti ule omwe an'bzicepsa pakati panupa, umweyo ndiye nkulu." |
1.206461 | Ainsi ont fait, avant eux, ceux qui ne croient pas. | " (Inu osakhulupirira) ndinu ofanana ndi amene adalipo patsogolo panu. |
1.206275 | Mais ils ont vraiment besoin de neuf ans pour le réparer, n'est-ce pas ? | Koma akufunikiradi zaka zisanu ndi zinayi kuti akonze, sichoncho? |
1.206125 | - Nous t'avons certes donné les sept versets que l'on répété, ainsi que le Coran sublime. | "Ndipo ndithu takupatsa (Ayah izi) zisanu ndi ziwiri zomawerenga kawirikawiri, (Sûrat Al-Fatihah), ndi Qur'an yolemekezeka. |
French-Chichewa_Sentence-Pairs Dataset
This dataset can be used for machine translation, sentence alignment, or other natural language processing tasks.
It is based on the NLLBv1 dataset, published on OPUS under an open-source initiative led by META. You can find more information here: OPUS - NLLB-v1
Metadata
- File Name: French-Chichewa_Sentence-Pairs
- File Size: 440963204 bytes
- Languages: French, French
Dataset Description
The dataset contains sentence pairs in African languages with an associated similarity score. The file is structured as a CSV with three columns:
similarity: The similarity score between the two sentences (range from 0 to 1).French: The first sentence in the pair.French: The second sentence in the pair.
This dataset is intended for use in training and evaluating machine learning models for tasks like translation, sentence similarity, and cross-lingual transfer learning.
References
Below are papers related to how the data was collected and used in various multilingual and cross-lingual applications:
[1] Holger Schwenk and Matthijs Douze, "Learning Joint Multilingual Sentence Representations with Neural Machine Translation", ACL workshop on Representation Learning for NLP, 2017
[2] Holger Schwenk and Xian Li, "A Corpus for Multilingual Document Classification in Eight Languages", LREC, pages 3548-3551, 2018.
[3] Holger Schwenk, "Filtering and Mining Parallel Data in a Joint Multilingual Space", ACL, July 2018
[4] Alexis Conneau, Guillaume Lample, Ruty Rinott, Adina Williams, Samuel R. Bowman, Holger Schwenk and Veselin Stoyanov, "XNLI: Cross-lingual Sentence Understanding through Inference", EMNLP, 2018.
[5] Mikel Artetxe and Holger Schwenk, "Margin-based Parallel Corpus Mining with Multilingual Sentence Embeddings", arXiv, Nov 3 2018.
[6] Mikel Artetxe and Holger Schwenk, "Massively Multilingual Sentence Embeddings for Zero-Shot Cross-Lingual Transfer and Beyond", arXiv, Dec 26 2018.
[7] Holger Schwenk, Vishrav Chaudhary, Shuo Sun, Hongyu Gong and Paco Guzman, "WikiMatrix: Mining 135M Parallel Sentences in 1620 Language Pairs from Wikipedia", arXiv, July 11 2019.
[8] Holger Schwenk, Guillaume Wenzek, Sergey Edunov, Edouard Grave and Armand Joulin, "CCMatrix: Mining Billions of High-Quality Parallel Sentences on the WEB", 2020.
[9] Paul-Ambroise Duquenne, Hongyu Gong, Holger Schwenk, "Multimodal and Multilingual Embeddings for Large-Scale Speech Mining", NeurIPS 2021, pages 15748-15761.
[10] Kevin Heffernan, Onur Celebi, and Holger Schwenk, "Bitext Mining Using Distilled Sentence Representations for Low-Resource Languages", 2022.
- Downloads last month
- 5